Tawbah – Kulapa

Tawbah – Kulapa

Ine ndapanga machimo ambiri  ndipo ndikufuna kubwelera kwa Allah ndikupanga tawba, kulapa koona. Kodi ndingapange bwanji tawbah imeneyi  Tawbah (Kulapa) ndi kokakamizidwa kwa Msilamu aliyense, ngakhaletu kwa makafiri. Munthu aliyense yem,we wafika msinkhu wolembedwa...
Dua Yopezera Banja

Dua Yopezera Banja

KODI PALI DUA YOPEZERA MWAMUNA/MKAZI WABANJA? Tidziwe kaye kuti dua ndi chani. Imeneyi ndi ibaadah komanso njira imodzi yodziyandikitsira kwa Allah chifukwa munthu umadzionetsa kwa Iye kuti popanda Iyeyo sungakhale kanthu. Ndiye munthu umapempha chilichonse poti mwini...
Mpango wa Kumutu si Hijab

Mpango wa Kumutu si Hijab

Mzimayi ndi okakamizidwa (Faradh) kubisa thupi lonse kupatula nkhope yake ndi manja ake. Ili ndi lamulo la Chisilamu lomwe mzimai wa Chisilamu akuyenera kutsatira ndipo palibe kupatula. Ena amanena kuti hijab ndi choice (kuisanklha kwawo)..ayi ndithu, kuteroko...
Istikhaarah – Kupempha Kusankha

Istikhaarah – Kupempha Kusankha

Kodi Istikhaarah ndi chani? Istikhaarah mu chiyankhulo cha Arabic Kumeneku ndi kupempha kusankha kwabwino pa chinthu. Amanena kuti: “pempha chisankho kwa Allah ﷻ , akusankhira”. Istikhaarah mu Deen Kupempha kusankha, kapena kuti kupempha kuti akuchotsere...
Fazail e Amaal (Fadhwaailul A’maal)

Fazail e Amaal (Fadhwaailul A’maal)

Buku la Fazail e Amaal (Fadhwailul A’maal) فضائل الأعمال “Maubwino a Ntchito za Bwino” “Sheikh Muhammad Zakariya Kandhlawi” download source Buku la Fadhaailul A’maal (فضائل الأعمال), lomwe pachiyambi linkatchedwa Tablighi...