Abale Athu Mchipembedzo

Abale Athu Mchipembedzo

Ngati makolo athu kapena abale athu ali ma kafir, tisawachite kukhala atetezi athu E inu amene mwakhulupirira! Musawachite makolo anu ndi abale anu kukhala atetezi anu ngati (iwo) akukonda kusakhulupirira Mulungu m’malo mokhulupirira (kukhala Asilamu). Ndipo mwa...
Malovu a Galu

Malovu a Galu

Ndi chifukwa chani timayenera kutsuka ndi mchenga kamodzi? “Kuyeretsa kwa chiwiya chanu chomwe wanyambitamo galu ndi kutsuka ka 7, kamodzi kakeko ndi mchenga”. Tonse tikudziwa kuti Mtumiki anatiuza kuti tidzitsuka chiwiya chomwe galu wanyambita ka seven,...
Ahlu Bayt…?

Ahlu Bayt…?

HUSSEIN .. MADAD YA HUSSEIN .. YA HUSSEIN !! Nchifukwa chani ma Shia amatamanda ndi kulemekeza Hussein (رضي الله عنه)  yekha ndi kusiya ana ena onse a Ali (رضي الله عنه)? Kodi munayamba mwazifunsapo funso limeneli? Nanga nkhani imeneyi inayamba yakudabwitsanipo?...
Nsembe ya Ismail

Nsembe ya Ismail

الحمد لله رب العالمين، والصلاة والسلام على رسوله الكريم وبعد Kuyamikidwa konse ndi kwa Mbuye wa zolengedwa zonse, yomwe anatipanga ife kukhala Asilamu nachipanga Chisilamu kukhala Chipembedzo chokhacho chomwe chidzalandiridwe pamaso pake.  Akunena mu Surah Aali Imraan...
Swalaat ya pa Mpando

Swalaat ya pa Mpando

Kukhala pa Mpando Poswali (Munthu yemwe akuloledwa kuswaali atakhala pampando akhale otani) 1. Akhale kuti akulephera kuimilira pa Swalaat Kuphatikiza kulephera kupanga rukuu’ ndi sajda molongosoka. Choncho aswali chokhala. Monga mmene Mtumiki salla Allah alaih...