Maina Abwino

Maina Abwino

Ena Mwa Maina Ololedwa Kuwapatsa Ana Athu Maina a Chimuna Abdul Latif Abdul Malik Abdul Raheem Abdul Rahman Abdul Salaam Abdul Samad, komanso maina onse a Mulungu, poyamba ndi liwu loti Abdul… Abu-Bakr Abdullah Adam Ahmad Akram Al Ameen Ali Ayyub Daud Dhakiyyu...
Maina Oletsedwa

Maina Oletsedwa

“Maina oletsedwa Kuwapatsa Ana Athu” zitsanzo za maina abwino Maina oyenera kuwapatsa ana athu MCHISILAMU akuyenera kukhala omwe ali abwino, KUPATULA awa: 1. Maina omwe ali ndi liwu la Ibaadah “Abdul-” kumayambiliro, nkulumikizidwa ndi maina...
Nkhani ya Mneneri Nooh (Noah) mtendere ukhale pa iye

Nkhani ya Mneneri Nooh (Noah) mtendere ukhale pa iye

Olemba: Sheikh Qullab T Jim Mneneri Nuhu (Nowa) ndi Mneneri wachiwiri kutumizidwa padziko lapansi pambuyo pa Mneneri Adam mwa Aneneri onse omwe Allah anawatumiza kwa anthu ndi cholinga chowawongelera ku njira yowongoka powayitanira iwo ku umodzi wa Mulungu (Tauhid),...
Imfa ya Munthu Okhulupilira ndi Osakhulupilira

Imfa ya Munthu Okhulupilira ndi Osakhulupilira

Nkhani inachokera kwa al-Bara’ ibn ‘Aazib yemwe anati: “tinapita ndi Mtumiki (Mtendere ndi Madalitso zipite kwa Iye) kumwambo woika mmanda mmodzi wa ma Ansar (mzika ya mumzinda wa Madina), ndipo titafika pa manda, tinapeza kuti sadaikidwe ku mphanga la manda. Kenako...
Mkazi Kuvala Buluku

Mkazi Kuvala Buluku

“Ndi zoletsedwa mu Chisilamu mkazi kuvala buluku (thalauza) lothina ndikuonetsa mmene thupi lake liliri. Ndipo chilango chake ndi choopsa zedi chifukwa mchitidwe umenewu umafalitsa machimo pa dziko.” Darul Iftail Misriy Allah anaika ndondomeko ya momwe...