by Kuunikira | May 23, 2022 | Featured, Kuunikira | 0 Comments
Wapita mwezi wa madalitso, Mwezi wa mapemphero, mwezi wa Qur'an, mwezi opeleka Chopeleka, Mwezi ochulukitsa zabwino, wapita basi mwezi umene oluza aluza opambana apambana, apambana amene adasala mwa chikhulupiliro natsatira ziphuzitso za Sharia zakusala, apambana...